Aefeso 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atamandike Mulungu, Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu,+ pakuti watidalitsa+ ndi dalitso lililonse lauzimu m’malo akumwamba+ mogwirizana ndi Khristu. 1 Petulo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anatibereka kuti tikhale ndi cholowa chosawonongeka,+ chosadetsedwa ndiponso chosasuluka. Cholowa chimenechi anasungira inuyo kumwamba,+
3 Atamandike Mulungu, Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu,+ pakuti watidalitsa+ ndi dalitso lililonse lauzimu m’malo akumwamba+ mogwirizana ndi Khristu.
4 Anatibereka kuti tikhale ndi cholowa chosawonongeka,+ chosadetsedwa ndiponso chosasuluka. Cholowa chimenechi anasungira inuyo kumwamba,+