Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 M’nyumba ya Atate wanga muli malo ambiri okhalamo.+ Akanapanda kukhalamo, ndikanakuuzani, chifukwa ndikupita kukakukonzerani malo.+

  • Aefeso 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 umene ndi chikole+ cha cholowa chathu cham’tsogolo,+ kuti anthu a Mulungu+ adzamasulidwe ndi dipo,+ n’cholinga choti iye adzatamandidwe ndi kupatsidwa ulemerero.

  • Akolose 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 chimene muli nacho chifukwa cha chiyembekezo+ chodzalandira zimene akusungirani kumwamba.+ Munamva za chiyembekezo chimenechi pamene choonadi cha uthenga wabwino chinalengezedwa kwa inu.+

  • 2 Timoteyo 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kuyambira panopa mpaka m’tsogolo, andisungira chisoti chachifumu chachilungamo.+ Ambuye, woweruza wolungama,+ adzandipatsa mphotoyo+ m’tsikulo.+ Sadzapatsa ine ndekha ayi, komanso onse amene akhala akuyembekezera kuti iye adzaonekere.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena