Aroma 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Si zokhazo ayi, komanso ifeyo amene tili ndi zipatso zoyambirira+ zomwe ndi mzimu, tikubuula+ mumtima mwathu pamene tikudikira ndi mtima wonse kuti titengedwe kukhala ana a Mulungu,+ kumasulidwa ndi dipo* kuti tituluke m’matupi athu. Akolose 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mwa Mwana wakeyo, tinamasulidwa ndi dipo,* kutanthauza kuti machimo athu anakhululukidwa.+ 1 Timoteyo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anadzipereka kuti akhale dipo* lokwanira ndendende m’malo mwa onse.+ Zimenezi ndi zimene adzazichitire umboni pa nthawi zake.
23 Si zokhazo ayi, komanso ifeyo amene tili ndi zipatso zoyambirira+ zomwe ndi mzimu, tikubuula+ mumtima mwathu pamene tikudikira ndi mtima wonse kuti titengedwe kukhala ana a Mulungu,+ kumasulidwa ndi dipo* kuti tituluke m’matupi athu.
6 Iye anadzipereka kuti akhale dipo* lokwanira ndendende m’malo mwa onse.+ Zimenezi ndi zimene adzazichitire umboni pa nthawi zake.