Agalatiya 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zinatero kuti amasule anthu okhala pansi pa chilamulo mwa kuwagula,+ kutinso Mulungu atitenge ife kukhala ana ake.+ Aefeso 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti anatisankhiratu+ kuti adzatitenga+ kukhala ana ake+ kudzera mwa Yesu Khristu, malinga ndi zomukomera iyeyo ndiponso chifuniro chake.+ 1 Petulo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anatibereka kuti tikhale ndi cholowa chosawonongeka,+ chosadetsedwa ndiponso chosasuluka. Cholowa chimenechi anasungira inuyo kumwamba,+ Chivumbulutso 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aliyense wopambana pa nkhondo adzalandira zimenezi monga cholowa. Ineyo ndidzakhala Mulungu wake,+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+
5 Zinatero kuti amasule anthu okhala pansi pa chilamulo mwa kuwagula,+ kutinso Mulungu atitenge ife kukhala ana ake.+
5 Pakuti anatisankhiratu+ kuti adzatitenga+ kukhala ana ake+ kudzera mwa Yesu Khristu, malinga ndi zomukomera iyeyo ndiponso chifuniro chake.+
4 Anatibereka kuti tikhale ndi cholowa chosawonongeka,+ chosadetsedwa ndiponso chosasuluka. Cholowa chimenechi anasungira inuyo kumwamba,+
7 Aliyense wopambana pa nkhondo adzalandira zimenezi monga cholowa. Ineyo ndidzakhala Mulungu wake,+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+