Aroma 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Popeza simunalandire mzimu wa ukapolo woyambitsanso mantha,+ koma munalandira mzimu+ wakuti mukhale ana,+ umene timafuula nawo kuti: “Abba,*+ Atate!” Aroma 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Amatero chifukwa amene anawadziwa choyamba+ anawasankhiratu+ kuti adzakhale ofanana+ ndi Mwana wake,+ kuti iye akhale woyamba kubadwa+ pakati pa abale ake ambiri.+ Agalatiya 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zinatero kuti amasule anthu okhala pansi pa chilamulo mwa kuwagula,+ kutinso Mulungu atitenge ife kukhala ana ake.+
15 Popeza simunalandire mzimu wa ukapolo woyambitsanso mantha,+ koma munalandira mzimu+ wakuti mukhale ana,+ umene timafuula nawo kuti: “Abba,*+ Atate!”
29 Amatero chifukwa amene anawadziwa choyamba+ anawasankhiratu+ kuti adzakhale ofanana+ ndi Mwana wake,+ kuti iye akhale woyamba kubadwa+ pakati pa abale ake ambiri.+
5 Zinatero kuti amasule anthu okhala pansi pa chilamulo mwa kuwagula,+ kutinso Mulungu atitenge ife kukhala ana ake.+