Salimo 89:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Inenso ndidzamuika kukhala mwana woyamba kubadwa,+Ndiponso mfumu yaikulu pa mafumu onse a padziko lapansi.+ Aheberi 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ponena za nthawi imene adzatumize kachiwiri Mwana wake Woyamba kubadwayo+ padziko lapansi kumene kuli anthu, iye akuti: “Angelo+ onse a Mulungu amugwadire.”+
27 Inenso ndidzamuika kukhala mwana woyamba kubadwa,+Ndiponso mfumu yaikulu pa mafumu onse a padziko lapansi.+
6 Koma ponena za nthawi imene adzatumize kachiwiri Mwana wake Woyamba kubadwayo+ padziko lapansi kumene kuli anthu, iye akuti: “Angelo+ onse a Mulungu amugwadire.”+