Salimo 91:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti adzalamula angelo ake za iwe,+Kuti akuteteze m’njira zako zonse.+ Luka 22:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Pamenepo mngelo wochokera kumwamba anaonekera kwa iye ndi kumulimbikitsa.+ Yohane 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atatero, anaona angelo awiri+ ovala zoyera, mmodzi atakhala pansi kumutu, winanso atakhala pansi kumiyendo, pamalo amene panagona mtembo wa Yesu.
12 Atatero, anaona angelo awiri+ ovala zoyera, mmodzi atakhala pansi kumutu, winanso atakhala pansi kumiyendo, pamalo amene panagona mtembo wa Yesu.