Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Choncho Mawu ameneyo anakhala ndi thupi+ la nyama ndi kukhala pakati pathu, ndipo tinaona ulemerero wake, ulemerero wa mwana wobadwa yekha+ kwa bambo ake. Anali wodzaza ndi kukoma mtima kwakukulu ndi choonadi.+

  • Yohane 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Wokhulupirira mwa iye sayenera kuweruzidwa.+ Wosakhulupirira waweruzidwa kale, chifukwa sanakhulupirire m’dzina la Mwana wobadwa yekha wa Mulungu.+

  • Aroma 8:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Amatero chifukwa amene anawadziwa choyamba+ anawasankhiratu+ kuti adzakhale ofanana+ ndi Mwana wake,+ kuti iye akhale woyamba kubadwa+ pakati pa abale ake ambiri.+

  • Akolose 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Iye ndiye chifaniziro+ cha Mulungu wosaonekayo,+ woyamba kubadwa+ wa chilengedwe chonse,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena