Yohane 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ine ndi Atate ndife amodzi.”+ Yohane 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yesu anati: “Anthu inu, ndakhala nanu nthawi yonseyi, koma kodi iwe Filipo sunandidziwebe? Amene waona ine waonanso Atate.+ Nanga iwe bwanji ukunena kuti, ‘Tionetseni Atate’?+ 2 Akorinto 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakati pa anthu amenewa, mulungu wa nthawi* ino+ wachititsa khungu maganizo a anthu osakhulupirira,+ kuti asaone+ kuwala+ kwa uthenga wabwino waulemerero+ wonena za Khristu, yemwe ali chifaniziro+ cha Mulungu.
9 Yesu anati: “Anthu inu, ndakhala nanu nthawi yonseyi, koma kodi iwe Filipo sunandidziwebe? Amene waona ine waonanso Atate.+ Nanga iwe bwanji ukunena kuti, ‘Tionetseni Atate’?+
4 Pakati pa anthu amenewa, mulungu wa nthawi* ino+ wachititsa khungu maganizo a anthu osakhulupirira,+ kuti asaone+ kuwala+ kwa uthenga wabwino waulemerero+ wonena za Khristu, yemwe ali chifaniziro+ cha Mulungu.