Deuteronomo 32:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Kondwerani, mitundu inu, pamodzi ndi anthu ake,+Pakuti adzabwezera magazi a atumiki ake,+Ndipo adzabwezera chilango kwa adani ake,+Nadzaphimba machimo a dziko la anthu ake.” Salimo 97:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Onse amene akupembedza chifaniziro chilichonse achite manyazi.+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yopanda pake achite manyazi.+Muweramireni, inu milungu yonse.+
43 Kondwerani, mitundu inu, pamodzi ndi anthu ake,+Pakuti adzabwezera magazi a atumiki ake,+Ndipo adzabwezera chilango kwa adani ake,+Nadzaphimba machimo a dziko la anthu ake.”
7 Onse amene akupembedza chifaniziro chilichonse achite manyazi.+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yopanda pake achite manyazi.+Muweramireni, inu milungu yonse.+