Deuteronomo 32:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndikanoladi lupanga langa lonyezimira,+Dzanja langa likagwira chiweruzo,+Ndidzalipsira adani anga,+Ndipo ndidzabwezera chilango kwa odana nane kwambiri.+ Mika 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndidzabwezera mokwiya ndiponso mwaukali mitundu ya anthu imene sinandimvere.”+ Luka 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 chifukwa amenewa ndi masiku obwezera chilango, kuti zonse zimene zinalembedwa zikwaniritsidwe.+
41 Ndikanoladi lupanga langa lonyezimira,+Dzanja langa likagwira chiweruzo,+Ndidzalipsira adani anga,+Ndipo ndidzabwezera chilango kwa odana nane kwambiri.+