Salimo 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngati munthu sadzabwerera kusiya zoipa,+ Mulungu adzanola lupanga lake,+Adzakunga uta wake ndi kukonzekera kulasa.+ Ezekieli 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Lupanga lanoledwa pokonzekera kupha anthu. Lapukutidwa kuti linyezimire.’”’”+ “Koma kodi tilibe chifukwa chosangalalira?”+ “‘Kodi lupangalo likukana ndodo yachifumu+ ya mwana wanga,+ ngati mmene likukanira mtengo uliwonse?+
12 Ngati munthu sadzabwerera kusiya zoipa,+ Mulungu adzanola lupanga lake,+Adzakunga uta wake ndi kukonzekera kulasa.+
10 Lupanga lanoledwa pokonzekera kupha anthu. Lapukutidwa kuti linyezimire.’”’”+ “Koma kodi tilibe chifukwa chosangalalira?”+ “‘Kodi lupangalo likukana ndodo yachifumu+ ya mwana wanga,+ ngati mmene likukanira mtengo uliwonse?+