Deuteronomo 32:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndikanoladi lupanga langa lonyezimira,+Dzanja langa likagwira chiweruzo,+Ndidzalipsira adani anga,+Ndipo ndidzabwezera chilango kwa odana nane kwambiri.+ Ezekieli 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Iwe mwana wa munthu, losera kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Nena mofuula kuti, ‘Lupanga! Lupanga!+ Lupanga lanoledwa+ ndi kupukutidwa.
41 Ndikanoladi lupanga langa lonyezimira,+Dzanja langa likagwira chiweruzo,+Ndidzalipsira adani anga,+Ndipo ndidzabwezera chilango kwa odana nane kwambiri.+
9 “Iwe mwana wa munthu, losera kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Nena mofuula kuti, ‘Lupanga! Lupanga!+ Lupanga lanoledwa+ ndi kupukutidwa.