Yesaya 66:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti ngati moto woyaka, Yehova adzaweruza anthu onse ndi lupanga lake,+ ndipo anthu ophedwa ndi Yehova adzakhala ambiri.+ Yeremiya 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu ofunkha adutsa m’njira zonse zodutsidwadutsidwa za m’chipululu. Lupanga la Yehova likuwononga anthu kuchokera kumalekezero a dziko kukafika kumalekezero ena a dziko.+ Palibe mtendere kwa munthu aliyense. Amosi 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akatengedwa ndi adani awo kupita ku ukapolo, kumeneko ndidzalamula lupanga kuti liwaphe.+ Ndidzakhala tcheru kuti ndiwagwetsere tsoka osati kuwapatsa madalitso.+
16 Pakuti ngati moto woyaka, Yehova adzaweruza anthu onse ndi lupanga lake,+ ndipo anthu ophedwa ndi Yehova adzakhala ambiri.+
12 Anthu ofunkha adutsa m’njira zonse zodutsidwadutsidwa za m’chipululu. Lupanga la Yehova likuwononga anthu kuchokera kumalekezero a dziko kukafika kumalekezero ena a dziko.+ Palibe mtendere kwa munthu aliyense.
4 Akatengedwa ndi adani awo kupita ku ukapolo, kumeneko ndidzalamula lupanga kuti liwaphe.+ Ndidzakhala tcheru kuti ndiwagwetsere tsoka osati kuwapatsa madalitso.+