Salimo 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngati munthu sadzabwerera kusiya zoipa,+ Mulungu adzanola lupanga lake,+Adzakunga uta wake ndi kukonzekera kulasa.+
12 Ngati munthu sadzabwerera kusiya zoipa,+ Mulungu adzanola lupanga lake,+Adzakunga uta wake ndi kukonzekera kulasa.+