Salimo 85:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tisonkhanitseni ndi kutibwezeretsa mwakale, inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Ndipo tichotsereni mkwiyo wanu.+ Yesaya 55:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu woipa asiye njira yake+ ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.+ Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+ Abwerere kwa Mulungu wathu, pakuti amakhululuka ndi mtima wonse.+ Malaki 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzatembenuza mitima ya abambo kuti ikhale ngati ya ana, ndipo adzatembenuza mitima ya ana kuti ikhale ngati ya abambo.* Adzachita zimenezi kuti ine ndisabwere kudzawononga dziko lapansi.”+ Luka 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye adzatembenuza ana ambiri a Isiraeli kuti abwerere kwa Yehova+ Mulungu wawo.
4 Tisonkhanitseni ndi kutibwezeretsa mwakale, inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Ndipo tichotsereni mkwiyo wanu.+
7 Munthu woipa asiye njira yake+ ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.+ Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+ Abwerere kwa Mulungu wathu, pakuti amakhululuka ndi mtima wonse.+
6 Iye adzatembenuza mitima ya abambo kuti ikhale ngati ya ana, ndipo adzatembenuza mitima ya ana kuti ikhale ngati ya abambo.* Adzachita zimenezi kuti ine ndisabwere kudzawononga dziko lapansi.”+