Salimo 85:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tibwezeretseni mwakale,* inu Mulungu amene mumatipulumutsa,Ndipo tichotsereni mkwiyo wanu.+