Salimo 80:3, 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Mulungu, tibwezeretseni mwakale.+Walitsani nkhope yanu pa ife kuti tipulumutsidwe.+ 4 Inu Yehova Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba, kodi mudzakwiyira* anthu anu nʼkukana kumvetsera mapemphero awo mpaka liti?+
3 Inu Mulungu, tibwezeretseni mwakale.+Walitsani nkhope yanu pa ife kuti tipulumutsidwe.+ 4 Inu Yehova Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba, kodi mudzakwiyira* anthu anu nʼkukana kumvetsera mapemphero awo mpaka liti?+