Salimo 74:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 74 Inu Mulungu, nʼchifukwa chiyani mwatikana mpaka kalekale?+ Nʼchifukwa chiyani mkwiyo wanu ukuyakira* nkhosa zimene mukuweta?+ Salimo 85:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi mutikwiyira mpaka kalekale?+ Kodi mudzapitiriza kusonyeza mkwiyo wanu ku mibadwomibadwo? Maliro 3:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mwadzitchinga ndi mtambo kuti pemphero lathu lisafike kwa inu.+
74 Inu Mulungu, nʼchifukwa chiyani mwatikana mpaka kalekale?+ Nʼchifukwa chiyani mkwiyo wanu ukuyakira* nkhosa zimene mukuweta?+