Salimo 74:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 74 Inu Mulungu, nʼchifukwa chiyani mwatikana mpaka kalekale?+ Nʼchifukwa chiyani mkwiyo wanu ukuyakira* nkhosa zimene mukuweta?+ Salimo 79:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova, kodi mukhala wokwiya mpaka liti? Kwamuyaya?+ Kodi mkwiyo wanu ukhala ukuyaka ngati moto mpaka liti?+
74 Inu Mulungu, nʼchifukwa chiyani mwatikana mpaka kalekale?+ Nʼchifukwa chiyani mkwiyo wanu ukuyakira* nkhosa zimene mukuweta?+
5 Inu Yehova, kodi mukhala wokwiya mpaka liti? Kwamuyaya?+ Kodi mkwiyo wanu ukhala ukuyaka ngati moto mpaka liti?+