Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 74:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 74 Inu Mulungu, nʼchifukwa chiyani mwatikana mpaka kalekale?+

      Nʼchifukwa chiyani mkwiyo wanu ukuyakira* nkhosa zimene mukuweta?+

  • Salimo 85:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Kodi mutikwiyira mpaka kalekale?+

      Kodi mudzapitiriza kusonyeza mkwiyo wanu ku mibadwomibadwo?

  • Yesaya 64:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Musatikwiyire kwambiri inu Yehova,+

      Ndipo musakumbukire zolakwa zathu kwamuyaya.

      Chonde, kumbukirani kuti tonsefe ndi anthu anu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena