Numeri 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova asonyeze kuti akusangalala nanu+ ndipo akukomereni mtima. Salimo 67:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Mulungu adzatikomera mtima ndi kutidalitsa.Iye adzasonyeza kuti akusangalala nafe+ (Selah) 2 Kuti njira zanu zidziwike padziko lonse lapansi,+Kuti mitundu yonse ya anthu idziwe kuti ndinu Mpulumutsi.+
67 Mulungu adzatikomera mtima ndi kutidalitsa.Iye adzasonyeza kuti akusangalala nafe+ (Selah) 2 Kuti njira zanu zidziwike padziko lonse lapansi,+Kuti mitundu yonse ya anthu idziwe kuti ndinu Mpulumutsi.+