Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 98:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Yehova wachititsa kuti chipulumutso chake chidziwike.+

      Wachititsa kuti anthu a mitundu yonse aone chilungamo chake.+

  • Yesaya 49:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ndiyeno iye anati: “Sikuti wangokhala mtumiki wanga

      Kuti ubwezeretse mafuko a Yakobo

      Ndiponso kuti Aisiraeli amene ali otetezeka uwabwezere kwawo.

      Koma ndakuperekanso kuti ukhale kuwala kwa anthu a mitundu ina,+

      Kuti chipulumutso changa chifike kumalekezero a dziko lapansi.”+

  • Luka 2:30, 31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 chifukwa maso anga aona njira yanu yopulumutsira anthu+ 31 imene mwakonza pamaso pa anthu a mitundu yonse.+

  • Machitidwe 28:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Choncho dziwani kuti njira ya Mulungu yopulumutsira anthu, yatumizidwa kwa anthu a mitundu ina.+ Ndipo mosakayikira, iwo adzamvetsera.”+

  • Tito 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mulungu waonetsa kukoma mtima kwake kwakukulu kumene kumabweretsa chipulumutso kwa anthu, kaya akhale otani.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena