Salimo 85:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tibwezeretseni mwakale,* inu Mulungu amene mumatipulumutsa,Ndipo tichotsereni mkwiyo wanu.+ Maliro 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu Yehova, tibwezereni kwa inu ndipo ife tibwerera kwa inu mwamsanga.+ Bwezeretsani zinthu zonse kuti zikhale ngati mmene zinalili kale.+
21 Inu Yehova, tibwezereni kwa inu ndipo ife tibwerera kwa inu mwamsanga.+ Bwezeretsani zinthu zonse kuti zikhale ngati mmene zinalili kale.+