Salimo 85:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tisonkhanitseni ndi kutibwezeretsa mwakale, inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Ndipo tichotsereni mkwiyo wanu.+
4 Tisonkhanitseni ndi kutibwezeretsa mwakale, inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Ndipo tichotsereni mkwiyo wanu.+