Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Pamapeto pake, zinthu zonsezi zikadzakuchitikirani nʼkukhala pamavuto aakulu, mudzabwerera kwa Yehova Mulungu wanu ndipo mudzamvera mawu ake.+

  • Salimo 80:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Inu Mulungu, tibwezeretseni mwakale.+

      Walitsani nkhope yanu pa ife kuti tipulumutsidwe.+

  • Salimo 85:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Tibwezeretseni mwakale,* inu Mulungu amene mumatipulumutsa,

      Ndipo tichotsereni mkwiyo wanu.+

  • Yeremiya 31:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Ndamva Efuraimu akulira kuti,

      ‘Ndinali ngati mwana wa ngʼombe wosaphunzitsidwa,

      Mwandidzudzula ndipo ndaphunzirapo kanthu.

      Ndithandizeni kuti ndibwerere ndipo ndidzabwereradi,

      Chifukwa inu ndinu Yehova Mulungu wanga.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena