Miyambo 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mumtima mwake muli zopotoka.+ Nthawi zonse amakhala akukonza zoipa.+ Amakhalira kuyambanitsa anthu.+ Yeremiya 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsuka mtima wako ndi kuchotsa zoipa zonse, iwe Yerusalemu, kuti upulumuke.+ Kodi maganizo ako oipawo udzakhala nawo mpaka liti?+ Yakobo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiye chilakolako chikatenga pakati, chimabala tchimo.+ Nalonso tchimo likakwaniritsidwa, limabweretsa imfa.+
14 Mumtima mwake muli zopotoka.+ Nthawi zonse amakhala akukonza zoipa.+ Amakhalira kuyambanitsa anthu.+
14 Tsuka mtima wako ndi kuchotsa zoipa zonse, iwe Yerusalemu, kuti upulumuke.+ Kodi maganizo ako oipawo udzakhala nawo mpaka liti?+
15 Ndiye chilakolako chikatenga pakati, chimabala tchimo.+ Nalonso tchimo likakwaniritsidwa, limabweretsa imfa.+