Ezekieli 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani! Miyoyo yonse ndi yanga.+ Moyo+ wa bambo komanso moyo wa mwana, yonse ndi yanga.+ Moyo umene ukuchimwawo+ ndi umene udzafe.+ Aroma 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa chiyani? Kuti mmene uchimo unalamulira monga mfumu pamodzi ndi imfa,+ momwemonso kukoma mtima kwakukulu+ kulamulire monga mfumu kudzera m’chilungamo. Zimenezi zichitike kuti moyo wosatha+ ubwere kudzera mwa Yesu Khristu Ambuye wathu. Aroma 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti chifukwa cha lamulo, uchimo unapeza njira yondinyenga+ ndipo unandipha.
4 Tamverani! Miyoyo yonse ndi yanga.+ Moyo+ wa bambo komanso moyo wa mwana, yonse ndi yanga.+ Moyo umene ukuchimwawo+ ndi umene udzafe.+
21 Chifukwa chiyani? Kuti mmene uchimo unalamulira monga mfumu pamodzi ndi imfa,+ momwemonso kukoma mtima kwakukulu+ kulamulire monga mfumu kudzera m’chilungamo. Zimenezi zichitike kuti moyo wosatha+ ubwere kudzera mwa Yesu Khristu Ambuye wathu.