Yohane 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Pakuti Mulungu anakonda+ kwambiri dziko mwakuti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense wokhulupirira+ iye asawonongeke,+ koma akhale ndi moyo wosatha.+ 1 Yohane 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mulungu anatisonyeza ife chikondi chake+ pakuti anatumiza m’dziko Mwana wake wobadwa yekha+ kuti tipeze moyo kudzera mwa iye.+
16 “Pakuti Mulungu anakonda+ kwambiri dziko mwakuti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense wokhulupirira+ iye asawonongeke,+ koma akhale ndi moyo wosatha.+
9 Mulungu anatisonyeza ife chikondi chake+ pakuti anatumiza m’dziko Mwana wake wobadwa yekha+ kuti tipeze moyo kudzera mwa iye.+