Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Pakuti Mulungu anakonda+ kwambiri dziko mwakuti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense wokhulupirira+ iye asawonongeke,+ koma akhale ndi moyo wosatha.+

  • Aroma 5:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Chifukwa chiyani? Kuti mmene uchimo unalamulira monga mfumu pamodzi ndi imfa,+ momwemonso kukoma mtima kwakukulu+ kulamulire monga mfumu kudzera m’chilungamo. Zimenezi zichitike kuti moyo wosatha+ ubwere kudzera mwa Yesu Khristu Ambuye wathu.

  • Aroma 8:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Iye amene sanaumire ngakhale Mwana wake+ koma anamupereka m’malo mwa ife tonse,+ angalephere bwanji kutipatsanso mokoma mtima zinthu zina zonse pamodzi ndi Mwana wakeyo?+

  • 1 Yohane 5:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Umboni umene waperekedwa ndi wakuti, Mulungu anatipatsa moyo wosatha,+ ndipo tinaulandira kudzera mwa Mwana wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena