Aroma 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Popeza sanaumire ngakhale Mwana wake koma anamupereka mʼmalo mwa ife tonse,+ angalephere bwanji kutipatsanso mokoma mtima zinthu zina zonse pamodzi ndi Mwana wakeyo? Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:32 Nsanja ya Olonda,10/15/2001, tsa. 14
32 Popeza sanaumire ngakhale Mwana wake koma anamupereka mʼmalo mwa ife tonse,+ angalephere bwanji kutipatsanso mokoma mtima zinthu zina zonse pamodzi ndi Mwana wakeyo?