Ekisodo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wachisomo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha+ ndi choonadi.+ 2 Mbiri 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Manase anayamba kupemphera kwa Mulungu ndipo iye anamva kupembedzera kwake+ ndi pempho lake lopempha chifundo. Kenako anam’bwezera ku Yerusalemu ku ufumu wake,+ ndipo Manase anadziwa kuti Yehova ndiye Mulungu woona.+ Salimo 103:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Monga mmene bambo amasonyezera chifundo kwa ana ake,+Yehova wasonyezanso chifundo kwa onse omuopa.+
6 Ndipo Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wachisomo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha+ ndi choonadi.+
13 Manase anayamba kupemphera kwa Mulungu ndipo iye anamva kupembedzera kwake+ ndi pempho lake lopempha chifundo. Kenako anam’bwezera ku Yerusalemu ku ufumu wake,+ ndipo Manase anadziwa kuti Yehova ndiye Mulungu woona.+
13 Monga mmene bambo amasonyezera chifundo kwa ana ake,+Yehova wasonyezanso chifundo kwa onse omuopa.+