Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 29:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Simunadye mkate,+ simunamwe vinyo ndi zakumwa zina zoledzeretsa, kuti mudziwe kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu.’

  • Salimo 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+

      Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+

      Higayoni.* [Seʹlah.]

  • Danieli 4:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Inuyo adzakuthamangitsani pakati pa anthu ndipo muzidzakhala pakati pa nyama zakutchire.+ Muzidzadya udzu ngati ng’ombe+ ndipo muzidzanyowa ndi mame akumwamba. Ndiyeno padzadutsa nthawi zokwanira 7+ kufikira mutadziwa kuti Wam’mwambamwamba ndiye Wolamulira wa maufumu a anthu,+ ndiponso kuti akafuna kupereka ulamuliro kwa munthu aliyense, amamupatsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena