Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 16:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Ndamva kung’ung’udza kwa ana a Isiraeli.+ Auze kuti, ‘Madzulo kuli kachisisira* mudzadya nyama, ndipo m’mawa mudzadya mkate ndi kukhuta.+ Pamenepo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”+

  • Ekisodo 16:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Chotero nyumba ya Isiraeli inayamba kutcha chakudyacho kuti “mana.”* Chinali choyera ngati njere ya mapira,* ndipo kukoma kwake kunali ngati makeke opyapyala othira uchi.+

  • Nehemiya 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Munawapatsanso mkate wochokera kumwamba kuti athetse njala yawo.+ Munatulutsa madzi pathanthwe ndi kuwapatsa kuti athetse ludzu lawo,+ ndiyeno munawauza kuti alowe+ ndi kutenga dziko limene munalumbira mutakweza dzanja lanu kuti mudzawapatsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena