Ekisodo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Popitiriza Mulungu anati: “Ukachite zimenezi kuti akakhulupirire kuti Yehova Mulungu wa makolo awo,+ Mulungu wa Abulahamu,+ Mulungu wa Isaki+ ndi Mulungu wa Yakobo,+ anaonekera kwa iwe.”+ Ekisodo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero ndidzakutengani kukhala anthu anga,+ ndi kukusonyezani kuti ndine Mulungu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndidzakutulutsani mu Iguputo, ndi kukuchotserani goli lawo.+ Ezekieli 34:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “‘Koma inu nkhosa zanga,+ nkhosa zimene ndikuzisamalira, ndinu anthu ochokera kufumbi. Ine ndine Mulungu wanu,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
5 Popitiriza Mulungu anati: “Ukachite zimenezi kuti akakhulupirire kuti Yehova Mulungu wa makolo awo,+ Mulungu wa Abulahamu,+ Mulungu wa Isaki+ ndi Mulungu wa Yakobo,+ anaonekera kwa iwe.”+
7 Chotero ndidzakutengani kukhala anthu anga,+ ndi kukusonyezani kuti ndine Mulungu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndidzakutulutsani mu Iguputo, ndi kukuchotserani goli lawo.+
31 “‘Koma inu nkhosa zanga,+ nkhosa zimene ndikuzisamalira, ndinu anthu ochokera kufumbi. Ine ndine Mulungu wanu,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”