Machitidwe 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Sitefano anati: “Amuna inu, abale anga ndi abambo anga, mvetserani! Mulungu waulemerero+ anaonekera kwa kholo lathu Abulahamu pamene anali ku Mesopotamiya, asanakakhale ku Harana.+ Aroma 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi lemba limati chiyani paja? Limati: “Abulahamu anakhulupirira mwa Yehova, ndipo anaonedwa ngati wolungama.”+
2 Sitefano anati: “Amuna inu, abale anga ndi abambo anga, mvetserani! Mulungu waulemerero+ anaonekera kwa kholo lathu Abulahamu pamene anali ku Mesopotamiya, asanakakhale ku Harana.+
3 Kodi lemba limati chiyani paja? Limati: “Abulahamu anakhulupirira mwa Yehova, ndipo anaonedwa ngati wolungama.”+