Ekisodo 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tamvera! Ine ndidzatsogola kukaima pathanthwe ku Horebe.* Kumeneko ukamenye thanthwelo, ndipo padzatuluka madzi amene anthu adzamwa.”+ Chotero Mose anachitadi zomwezo, pamaso pa akulu a Isiraeli, Salimo 78:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Taonani! Kodi Mulungu si uja anamenya thanthwe+Kuti madzi atuluke, kutinso patuluke mitsinje yodzaza madzi?+Koma iwo anati: “Kodi angathenso kutipatsa chakudya,+Kapena kodi angakonzere anthu ake chakudya?”+
6 Tamvera! Ine ndidzatsogola kukaima pathanthwe ku Horebe.* Kumeneko ukamenye thanthwelo, ndipo padzatuluka madzi amene anthu adzamwa.”+ Chotero Mose anachitadi zomwezo, pamaso pa akulu a Isiraeli,
20 Taonani! Kodi Mulungu si uja anamenya thanthwe+Kuti madzi atuluke, kutinso patuluke mitsinje yodzaza madzi?+Koma iwo anati: “Kodi angathenso kutipatsa chakudya,+Kapena kodi angakonzere anthu ake chakudya?”+