Ekisodo 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ndamva kungʼungʼudza kwa Aisiraeli.+ Ndiye uwauze kuti, ‘Madzulo kuli kachisisira* mudzadya nyama ndipo mʼmawa mudzadya mkate nʼkukhuta.+ Pamenepo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”+
12 “Ndamva kungʼungʼudza kwa Aisiraeli.+ Ndiye uwauze kuti, ‘Madzulo kuli kachisisira* mudzadya nyama ndipo mʼmawa mudzadya mkate nʼkukhuta.+ Pamenepo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”+