Miyambo 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ngati wakodwa ndi mawu a m’kamwa mwako,+ ngati wagwidwa ndi mawu a m’kamwa mwako, Miyambo 26:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Amene akukumba dzenje adzagweramo yekha,+ ndipo amene akugubuduza mwala udzabwerera kwa iye.+ Yesaya 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsoka kwa anthu oipa! Iwo adzaona zoopsa, chifukwa zimene anachitira ena ndi manja awo, zidzawachitikira iwowo.+
11 Tsoka kwa anthu oipa! Iwo adzaona zoopsa, chifukwa zimene anachitira ena ndi manja awo, zidzawachitikira iwowo.+