Salimo 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye wafukula dzenje, walikumbadi.+Koma adzagwera m’dzenje lokumba yekha.+ Salimo 57:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwo anditchera ukonde panjira yanga.+Moyo wanga wagwidwa ndi chisoni.+Andikumbira mbuna.Koma iwo agweramo.+ [Seʹlah.] Miyambo 28:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu amene amasocheretsa anthu owongoka mtima+ kuti ayende m’njira yoipa, adzagwera m’dzenje lake lomwe.+ Koma anthu osalakwa adzapeza zabwino.+
6 Iwo anditchera ukonde panjira yanga.+Moyo wanga wagwidwa ndi chisoni.+Andikumbira mbuna.Koma iwo agweramo.+ [Seʹlah.]
10 Munthu amene amasocheretsa anthu owongoka mtima+ kuti ayende m’njira yoipa, adzagwera m’dzenje lake lomwe.+ Koma anthu osalakwa adzapeza zabwino.+