Esitere 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho anapachika Hamani pamtengo+ umene anakonzera Moredekai,+ ndipo mkwiyo wa mfumu unatha. Salimo 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Modzikweza, woipa amathamangitsa wosautsika,+Ndipo wosautsikayo amakodwa ndi maganizo amene woipa walingalira.+ Miyambo 26:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Amene akukumba dzenje adzagweramo yekha,+ ndipo amene akugubuduza mwala udzabwerera kwa iye.+
2 Modzikweza, woipa amathamangitsa wosautsika,+Ndipo wosautsikayo amakodwa ndi maganizo amene woipa walingalira.+