Salimo 37:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yembekezera Yehova, ndi kusunga njira zake,+Ndipo adzakukweza kuti ulandire dziko lapansi.+Pamene oipa akuphedwa, iwe udzaona.+ Miyambo 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu woipa ndiye dipo la wolungama,+ ndipo munthu wochita zachinyengo amalowa m’malo mwa anthu owongoka mtima.+ 2 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+
34 Yembekezera Yehova, ndi kusunga njira zake,+Ndipo adzakukweza kuti ulandire dziko lapansi.+Pamene oipa akuphedwa, iwe udzaona.+
18 Munthu woipa ndiye dipo la wolungama,+ ndipo munthu wochita zachinyengo amalowa m’malo mwa anthu owongoka mtima.+
9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+