Salimo 52:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Olungama adzaona zimenezi ndi kuchita mantha,+Ndipo adzamuseka.+ Salimo 91:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Udzayang’ana ndi maso ako,+Ndipo udzaona anthu oipa akulandira chilango.+