Salimo 37:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yembekezera Yehova, ndi kusunga njira zake,+Ndipo adzakukweza kuti ulandire dziko lapansi.+Pamene oipa akuphedwa, iwe udzaona.+ Malaki 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu mudzaona zimenezi ndi maso anu ndipo mudzati: “Yehova atamandike m’dera lonse la Isiraeli.”’”+
34 Yembekezera Yehova, ndi kusunga njira zake,+Ndipo adzakukweza kuti ulandire dziko lapansi.+Pamene oipa akuphedwa, iwe udzaona.+