Salimo 35:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo andikumbira mbuna popanda chifukwa ndi kuikapo ukonde,+Akumba mbunazo kuti ndigweremo ngakhale kuti sindinalakwe.+ Salimo 40:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye ananditulutsanso m’dzenje la madzi a mkokomo,+Ananditulutsa m’chithaphwi cha matope.+Kenako anapondetsa phazi langa pathanthwe.+Anandiyendetsa panthaka yolimba.+ Salimo 57:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwo anditchera ukonde panjira yanga.+Moyo wanga wagwidwa ndi chisoni.+Andikumbira mbuna.Koma iwo agweramo.+ [Seʹlah.] Yeremiya 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi zabwino amazibwezera ndi zoipa?+ Kumbukirani nthawi zonse zija pamene ndinaima pamaso panu kuwalankhulira zabwino kuti muwachotsere mkwiyo wanu.+ Koma iwo tsopano andikumbira mbuna.+
7 Iwo andikumbira mbuna popanda chifukwa ndi kuikapo ukonde,+Akumba mbunazo kuti ndigweremo ngakhale kuti sindinalakwe.+
2 Iye ananditulutsanso m’dzenje la madzi a mkokomo,+Ananditulutsa m’chithaphwi cha matope.+Kenako anapondetsa phazi langa pathanthwe.+Anandiyendetsa panthaka yolimba.+
6 Iwo anditchera ukonde panjira yanga.+Moyo wanga wagwidwa ndi chisoni.+Andikumbira mbuna.Koma iwo agweramo.+ [Seʹlah.]
20 Kodi zabwino amazibwezera ndi zoipa?+ Kumbukirani nthawi zonse zija pamene ndinaima pamaso panu kuwalankhulira zabwino kuti muwachotsere mkwiyo wanu.+ Koma iwo tsopano andikumbira mbuna.+