Salimo 35:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo andikumbira mbuna popanda chifukwa ndi kuikapo ukonde,+Akumba mbunazo kuti ndigweremo ngakhale kuti sindinalakwe.+ Salimo 57:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwo anditchera ukonde panjira yanga.+Moyo wanga wagwidwa ndi chisoni.+Andikumbira mbuna.Koma iwo agweramo.+ [Seʹlah.] Mlaliki 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amene akukumba dzenje adzagweramo,+ ndipo amene akugumula mpanda wamiyala njoka idzamuluma.+
7 Iwo andikumbira mbuna popanda chifukwa ndi kuikapo ukonde,+Akumba mbunazo kuti ndigweremo ngakhale kuti sindinalakwe.+
6 Iwo anditchera ukonde panjira yanga.+Moyo wanga wagwidwa ndi chisoni.+Andikumbira mbuna.Koma iwo agweramo.+ [Seʹlah.]