Salimo 109:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikawachitira zabwino amandibwezera zoipa,+Ndikawasonyeza chikondi amandibwezera chidani.+