Salimo 35:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo andikumbira mbuna popanda chifukwa ndi kuikapo ukonde,+Akumba mbunazo kuti ndigweremo ngakhale kuti sindinalakwe.+ Salimo 38:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwo anali kundibwezera choipa m’malo mwa chabwino,+Ndikamayesetsa kuchita chabwino anali kunditsutsa.+ Miyambo 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Aliyense wobwezera zoipa pa zabwino,+ zoipa sizidzachoka panyumba pake.+
7 Iwo andikumbira mbuna popanda chifukwa ndi kuikapo ukonde,+Akumba mbunazo kuti ndigweremo ngakhale kuti sindinalakwe.+
20 Iwo anali kundibwezera choipa m’malo mwa chabwino,+Ndikamayesetsa kuchita chabwino anali kunditsutsa.+