1 Samueli 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Davide anali atanena kuti: “Ine ndinalondera zinthu zake m’chipululu ndipo palibe chinthu chake ngakhale chimodzi chimene chinasowa.+ N’zokhumudwitsa kuti munthu ameneyu akundibwezera zoipa pa zabwino zimene ndinam’chitira.+ Salimo 35:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Adani anga amandibwezera zoipa m’malo mwa zabwino,+Ndipo ndimakhala wachisoni ngati wofedwa.+ Yeremiya 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi zabwino amazibwezera ndi zoipa?+ Kumbukirani nthawi zonse zija pamene ndinaima pamaso panu kuwalankhulira zabwino kuti muwachotsere mkwiyo wanu.+ Koma iwo tsopano andikumbira mbuna.+
21 Davide anali atanena kuti: “Ine ndinalondera zinthu zake m’chipululu ndipo palibe chinthu chake ngakhale chimodzi chimene chinasowa.+ N’zokhumudwitsa kuti munthu ameneyu akundibwezera zoipa pa zabwino zimene ndinam’chitira.+
20 Kodi zabwino amazibwezera ndi zoipa?+ Kumbukirani nthawi zonse zija pamene ndinaima pamaso panu kuwalankhulira zabwino kuti muwachotsere mkwiyo wanu.+ Koma iwo tsopano andikumbira mbuna.+