1 Samueli 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ine ndamva kuti ukumeta ubweya wa nkhosa zako. Abusa ako anali ndi ife.+ Sitinawavutitse,+ ndipo masiku onse amene tinali nawo ku Karimeli, palibe kanthu kawo kamene kanasowa.
7 Ine ndamva kuti ukumeta ubweya wa nkhosa zako. Abusa ako anali ndi ife.+ Sitinawavutitse,+ ndipo masiku onse amene tinali nawo ku Karimeli, palibe kanthu kawo kamene kanasowa.